Psalms 29:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amagwedeza phiri la Lebanoni kuti lizivinavina ngati likonyani, amavinitsa phiri la Sirioni ngati mwanawanjati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aitumphitsa monga mwanawang'ombe; Lebanoni ndi Sirioni monga msona wa njati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amachititsa Lebanoni kulumphalumpha ngati mwana wangʼombe, Siriyoni ngati mwana wa njati:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aitumphitsa monga mwana wa ng'ombe; Lebano ndi Sirio monga msona wa njati.