Psalms 3:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, ndili ndi adani ochuluka, anthu ambiri akundiwukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Davide, muja anathawa Abisalomu mwana wake. Yehova! Ha! Achuluka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Atathawa mwana wake Abisalomu. Inu Yehova, achulukadi adani anga! Achulukadi amene andiwukira!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova! Ha! acuruka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri.