Psalms 3:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Inu Chauta, ndinu chishango changa chonditeteza, ndinu ulemerero wanga, mumalimbitsa mtima wanga ndinu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Inu Yehova, ndinu chikopa changa; ulemerero wanga, ndi wondiweramutsa mutu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Yehova, ndinu chishango chonditeteza, Inu mwandiveka ulemerero ndipo mwanditukula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Inu Yehova, ndinu cikopa canga; Ulemerero wanga, ndi wondiweramutsa mutu wanga.