Psalms 3:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimagona ndipo ndimapeza tulo. Ndimadzukanso m'maŵa pakuti Chauta amanditchinjiriza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinagona ine pansi, ndinagona tulo; ndinauka; pakuti Yehova anandichirikiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndimagona ndi kupeza tulo; ndimadzukanso chifukwa Yehova amandichirikiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinagona ine pansi, ndinagona tulo; Ndinauka; pakuti Yehova anandicirikiza.