Psalms 30:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwasandutsa kulira kwanga kuti kukhale kuvina, mwachotsa chisoni changa ndi kundipatsa chisangalalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munasanduliza kulira kwanga kukhale kusekera; munandivula chiguduli changa, ndipo munandiveka chikondwero,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munasandutsa kulira kwanga kukhala kuvina; munachotsa chiguduli changa ndi kundiveka ndi chimwemwe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munasanduliza kulira kwanga kukhale kusekera; Munandibvula ciguduli canga, ndipo munandibveka cikondwero: