Psalms 30:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta, Mulungu wanga, ndidalirira Inu kuti mundithandize, ndipo mwandichiritsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, Mulungu wanga, ndinafuulira kwa Inu, ndipo munandichiritsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova Mulungu wanga ndinapempha kwa Inu thandizo ndipo Inu munandichiritsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, Mulungu wanga, Ndinapfuulira kwa Inu, ndipo munandiciritsa.