Psalms 30:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, mwanditulutsa m'dziko la akufa, mwandibwezeranso moyo kuti ndingatsikire ku manda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova munabweza moyo wanga kumanda, munandisunga ndi moyo, kuti ndingatsikire kudzenje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, munanditulutsa ku manda, munandisunga kuti ndisatsalire mʼdzenje.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova munabweza moyo wanga kumanda: Munandisunga ndi moyo, kuti ndingatsikire kudzenje.