Psalms 30:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine, pamene zinthu zidaandiyendera bwino, ndidati, “Sindidzagwedezeka konse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ine, ndinanena m'phindu langa, sindidzagwedezeka nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndinaona kuti ndili otetezedwa ndinati, “Sindidzagwedezekanso.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ine, ndinanena m'phindu langa, Sindidzagwedezeka nthawi zonse.