Psalms 30:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha kukoma mtima kwanu, Inu Chauta, mudandikhazikitsa ngati phiri lolimba. Koma pamene mudandimana madalitso anu, ine ndidataya mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu, Yehova, munakhazikitsa phiri langa ndi kuyanja kwanu; munabisa nkhope yanu; ndinaopa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, pamene munandikomera mtima, munachititsa phiri langa kuyima chilili; koma pamene munabisa nkhope yanu, ndinataya mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu, Yehova, munakhazikitsa phiri langa ndi kuyanja kwanu: Munabisa nkhope yanu; ndinaopa.