Psalms 30:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo ndidalirira Inu Chauta, ndipo ndidapempha chifundo chanu kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinafuulira kwa Inu, Yehova; kwa Yehova ndinapemba,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa Inu Yehova ndinayitana; kwa Ambuye ndinapempha chifundo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinapfuulira kwa Inu, Yehova; Kwa Yehova ndinapemba: