Psalms 31:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, ndimamva anthu ambiri akunong'onezana zoipa za ine, zoopsa zandizinga ponseponse. Amapangana zoti andiwukire, namachita upo woipa woti andiphe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndamva ugogodi wa ambiri, mantha andizinga. Pondipangira chiwembu, anatsimikiza mtima kulanda moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ine ndamva zonena zoyipa za anthu ambiri; zoopsa zandizungulira mbali zonse; iwo akukonza chiwembu kuti alimbane nane, kuti atenge moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndamva ugogodi wa ambiri, Mantha andizinga: Pondipangira ciwembu, Anatsimikiza mtima kulanda moyo wanga.