Psalms 31:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndimadalira Inu Chauta, ndimati, “Inu ndinu Mulungu wanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine ndakhulupirira Inu, Yehova, ndinati, Inu ndinu Mulungu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ndikudalira Inu Yehova; ndikunena kuti, “Ndinu Mulungu wanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine ndakhulupirira Inu, Yehova: Ndinati, Inu ndinu Mulungu wanga,