Psalms 31:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, musalole kuti ndichite manyazi, chifukwa ndapemphera kwa Inu. Koma anthu oipa ndiwo achite manyazi, apite ku manda kachetechete.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, musandichititse manyazi; pakuti ndafuulira kwa Inu, oipa achite manyazi, atonthole m'manda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndalirira kwa Inu; koma oyipa achititsidwe manyazi ndipo agone chete mʼmanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, musandicititse manyazi; pakuti ndapfuulira kwa Inu: Oipa acite manyazi, atonthole m'manda.