Psalms 31:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onse onyada ndi onama olankhula mwamwano ndi monyoza kwa anthu abwino, muŵakhalitse chete.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ikhale yosalankhula milomo ya mabodza, imene imalankhula mwachipongwe pa olungama mtima, ndi kudzikuza ndi kunyoza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Milomo yawo yabodzayo ikhale chete, pakuti chifukwa cha kunyada ayankhula modzikuza kutsutsana ndi wolungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ikhale yosalankhula milomo ya mabodza, Imene imalankhula mwacipongwe pa olungama mtima, Ndi kudzikuza ndi kunyoza.