Psalms 31:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi waukulu ubwino wanu umene mwaŵasungira anthu okumverani, umene mwaŵachitira anthu othaŵira kwa Inu, aliyense waona zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha! Kukoma kwanu ndiko kwakukulu nanga, kumene munasungira iwo akuopa Inu, kumene munachitira iwo akukhulupirira Inu, pamaso pa ana a anthu!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi waukulu ubwino wanu umene mwawasungira amene amakuopani, umene mumapereka anthu akuona kwa iwo amene amathawira kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha! kukoma kwanu ndiko kwakukuru nanga, kumene munasungira iwo akuopa Inu, Kumene munacitira iwo akukhulupirira Inu, pamaso pa ana a anthu!