Psalms 31:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidalankhula mwankhaŵa kuti, “Andipirikitsira kutali ndi Inu.” Koma Inu mudamva kupempha kwanga pamene ndidakudandaulirani kuti mundithandize.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ine, pakutenga nkhawa, ndinati, Ndadulidwa kundichotsa pamaso panu. Komatu munamva mau a kupemba kwanga pamene ndinafuulira kwa Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndili mʼnkhawa zanga ndinati, “Ine ndachotsedwa pamaso panu!” Komabe Inu munamva kupempha chifundo kwanga pamene ndinapempha thandizo kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ine, pakutenga nkhawa, ndinati, Ndadulidwa kundicotsa pamaso panu: Komatu munamva mau a kupemba kwanga pamene ndinapfuulira kwa Inu.