Psalms 31:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikupereka moyo wanga m'manja mwanu. Inu Chauta wokhulupirika, mwandiwombola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipereka mzimu wanga m'dzanja lanu; mwandiombola, Inu Yehova, Mulungu wa choonadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmanja mwanu ndipereka mzimu wanga; womboleni Yehova Mulungu wachoonadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipereka mzimu wanga m'dzanja lanu: Mwandiombola, Inu Yehova, Mulungu wa coonadi.