Psalms 31:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumadana ndi opembedza mafano achabechabe. Koma ine ndimakhulupirira Inu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikwiya nao iwo akusamala zachabe zonama, koma ndikhulupirira Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ine ndimadana nawo amene amamamatira mafano achabechabe; ine ndimadalira Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikwiya nao iwo akusamala zacabe zonama: Koma ndikhulupirira Yehova.