Psalms 31:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakondwa ndi kusangalala chifukwa ndinu a chikondi chosasinthika. Mwaona masautso anga, mwazindikira mavuto anga kuti ndi aakulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakondwera ndi kusangalala m'chifundo chanu, pakuti mudapenya zunzo langa; ndipo mudadziwa mzimu wanga mu nsautso yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakondwa ndi kusangalala mʼchikondi chanu popeza Inu munaona masautso anga ndipo mumadziwa kuwawa kwa moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakondwera ndi kusangalala m'cifundo canu: Pakuti mudapenya zunzo langa; Ndipo mudadziwa mzimu wanga mu nsautso yanga: