Psalms 31:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Simudandipereke m'manja mwa adani anga, koma mwandiika pa malo otambalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo simunandipereka m'dzanja la mdani; munapondetsa mapazi anga pali malo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu simunandipereke kwa mdani koma mwayika mapazi anga pa malo otakasuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo simunandipereka m'dzanja la mdani; Munapondetsa mapazi anga pali malo.