Psalms 32:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sangalalani ndi kukondwa inu nonse okonda Mulungu, chifukwa cha zimene Chautayo adakuchitirani. Inu anthu ake onse, fuulani ndi chimwemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sekerani mwa Yehova, ndimo kondwerani inu olungama mtima; ndipo fuulani mokondwera nonsenu oongoka mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kondwerani mwa Yehova inu olungama; imbani, inu nonse amene muli owongoka mtima!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sekerani mwa Yehova, ndimo kondwerani inu olungama mtima; Ndipo pfuulani mokondwera nonsenu oongoka mtima.