Psalms 32:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndinali ndisanaulule tchimo langa, thupi langa linali lofooka, chifukwa cha kubuula tsiku lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene ndinakhala chete mafupa anga anakalamba ndi kubuula kwanga tsiku lonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndinali chete, mafupa anga anakalamba chifukwa cha kubuwula kwanga tsiku lonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene ndinakhala cete mafupa anga anakalamba Ndi kubuula kwanga tsiku lonse.