Psalms 32:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti usana ndi usiku dzanja lanu lidandipsinja, motero nyonga zanga zidatha, monga amafotera masamba ndi dzuŵa lachilimwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa usana ndi usiku dzanja lanu linandilemera ine; uwisi wanga unasandulika kuuma kwa malimwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti usana ndi usiku dzanja lanu linandipsinja; mphamvu zanga zinatha monga nthawi yotentha yachilimwe. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa usana ndi usiku dzanja lanu linandilemera ine; Uwisi wanga unasandulika kuuma kwa malimwe.