Psalms 32:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu ndinu kobisalira kwanga. Inu mumanditchinjiriza nthaŵi yamavuto. Nchifukwa chake ndimaimba nyimbo zotamanda chipulumutso chanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu ndinu mobisalira mwanga; m'nsautso mudzandisunga; mudzandizinga ndi nyimbo za chipulumutso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu ndi malo anga obisala; muzinditeteza ku mavuto ndipo muzindizinga ndi nyimbo zachipulumutso. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu ndinu mobisalira mwanga; M'nsautso mudzandisunga; Mudzandizinga ndi Nyimbo za cipulumutso.