Psalms 32:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Musakhale opanda nzeru ngati kavalo kapena bulu amene ayenera kumuwongolera ndi chitsulo cham'kamwa ndi chapamutu, chifukwa ukapanda kutero, nyamazo sizidzakumvera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musakhale monga kavalo, kapena ngati bulu, wopanda nzeru; zomangira zao ndizo cham'kamwa ndi chapamutu zakuwakokera, pakuti ukapanda kutero sadzakuyandikiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usakhale ngati kavalo kapena bulu, zimene zilibe nzeru, koma ziyenera kuwongoleredwa ndi zitsulo za mʼkamwa ndi pamutu, ukapanda kutero sizibwera kwa iwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musakhale monga kavalo, kapena ngati buru, wopanda nzeru: Zomangira zao ndizo cam'kamwa ndi capamutu zakuwakokera, Pakuti ukapanda kutero sadzakuyandikiza.