Psalms 33:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngwodala mtundu wa anthu amene Mulungu wao ndi Chauta, anthu amene Chauta waŵasankha akeake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodalitsika mtundu wa anthu umene Yehova ndiye Mulungu wao; mtundu womwe anausankha ukhale cholandira cha Iye yekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wodala mtundu wa anthu umene Mulungu wake ndi Yehova, anthu amene Iye anawasankha kukhala cholowa chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodalitsika mtundu wa anthu umene Yehova ndiye Mulungu wao; Mtundu womwe anausankha ukhale colandira ca iye yekha.