Psalms 33:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ali kumwamba, amayang'ana pansi ndi kuwona anthu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova apenyerera m'mwamba; aona ana onse a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera kumwamba Yehova amayangʼana pansi ndi kuona anthu onse;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova apenyerera m'mwamba; Aona ana onse a anthu.