Psalms 33:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu siipulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake la ankhondo. Wankhondo sapulumuka chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Palibe mfumu yoti gulu lalikulu limpulumutsa, mphamvu yaikulu siichilanditsa chiphona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe mfumu imene imapulumutsidwa chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo; palibe msilikali amene amathawa ndi mphamvu zake zazikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Palibe mfumu yoti gulu lalikuru limpulumutsa: Mphamvu yaikuru siicilanditsa ciphona,