Psalms 33:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa kavalo wankhondo sungaikepo mtima kuti upambane, chifukwa sangathe kupulumutsa munthu, ngakhale kavaloyo ali ndi mphamvu zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kavalo safikana kupulumuka naye, chinkana mphamvu yake njaikulu sapulumutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kavalo ndi chiyembekezo cha chabechabe cha chipulumutso, ngakhale ali ndi mphamvu yayikulu sangathe kupulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kavalo safikana kupulumuka naye: Cinkana mphamvu yace njaikuru sapulumutsa.