Psalms 33:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amayang'ana anthu omumvera, ndi odalira chikondi chake chosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, diso la Yehova lili pa iwo akumuopa Iye, pa iwo akuyembekeza chifundo chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma maso a Yehova ali pa iwo amene amaopa Iye; amene chiyembekezo chawo chili mʼchikondi chake chosatha,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, diso la Yehova liri pa iwo akumuopa Iye, Pa iwo akuyembekeza cifundo cace;