Psalms 33:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye amachita izi kuti aŵapulumutse ku imfa ndi kuŵasungira moyo anthuwo pa nthaŵi ya njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kupulumutsa moyo wao kwa imfa, ndi kuwasunga ndi moyo m'nyengo ya njala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuwawombola iwo ku imfa ndi kuwasunga ndi moyo nthawi ya njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kupulumutsa moyo wao kwa imfa, Ndi kuwasunga ndi moyo m'nyengo ya njala.