Psalms 33:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamandani Chauta ndi pangwe. Muimbireni nyimbo ndi zeze wa nsambo khumi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yamikani Yehova ndi zeze; muimbireni ndi chisakasa cha zingwe khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mutamandeni Yehova ndi pangwe; muyimbireni Iye nyimbo pa zeze wa zingwe khumi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yamikani Yehova ndi zeze: Myimbireni ndi cisakasa ca zingwe khumi.