Psalms 33:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitima yathu imasangalala mwa Chauta, popeza kuti timadalira dzina lake loyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mtima wathu udzakondwera mwa Iye, chifukwa takhulupirira dzina lake loyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa Iye mitima yathu imakondwera, pakuti ife timadalira dzina lake loyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mtima wathu udzakondwera mwa Iye, Cifukwa takhulupirira dzina lace loyera.