Psalms 33:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, chikondi chanu chosasinthika chikhale pa ife, chifukwa timakhulupirira Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, chifundo chanu chikhale pa ife, monga takuyembekezani Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikondi chanu chosatha chikhale pa ife Inu Yehova, pamene tikuyembekeza kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, cifundo canu cikhale pa ife, Monga takuyembekezani Inu.