Psalms 33:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalankhula ndipo zakumwamba zidalengedwa. Zonse zakumeneko zidalengedwa pamene Iye adalankhula mau ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zakumwamba zinalengedwa ndi mau a Yehova; ndipo ndi mpweya wa m'kamwa mwake khamu lao lonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi mawu a Yehova mayiko akumwamba anapangidwa, zolengedwa zake ndi mpweya wa mʼkamwa mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zakumwamba zinalengedwa ndi mau a Yehova; Ndipo ndi mpweya wa m'kamwa mwace khamu lao lonse.