Psalms 33:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lonse lapansi liwope Chauta. Anthu onse okhala pa dziko lapansi achite naye mantha,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko lonse lapansi liope Yehova, ponse pali anthu achite mantha chifukwa cha Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko lonse lapansi liope Yehova; anthu onse amulemekeze Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lonse lapansi liope Yehova: Ponse pali anthu acite mantha cifukwa ca Iye,