Psalms 34:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale anaamkango amasoŵa chakudya ndipo amakhala anjala, koma anthu amene amalakalaka Chauta, sasoŵa zinthu zabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Misona ya mkango isowa nimva njala, koma iwo akufuna Yehova sadzasowa kanthu kabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikango itha kulefuka ndi kumva njala koma iwo amene amafunafuna Yehova sasowa kanthu kalikonse kabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Misona ya mkango isowa nimva njala: Koma iwo akufuna Yehova sadzasowa kanthu kabwino.