Psalms 34:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani mwa inu amakhumba moyo ndi kulakalaka kuti akhale masiku ambiri, kuti asangalale ndi zinthu zabwino?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu wokhumba moyo ndani, wokonda masiku, kuti aone zabwino?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense wa inu amene amakonda moyo wake ndi kukhumba kuti aone masiku abwino ambiri,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu wokhumba moyo ndani, Wokonda masiku, kuti aone zabwino?