Psalms 34:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta amaŵakwiyira anthu ochita zoipa, anthuwo sadzakumbukikanso pansi pano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nkhope ya Yehova itsutsana nao akuchita zoipa, kudula chikumbukiro chao pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nkhope ya Yehova ikutsutsana ndi amene amachita zoyipa, kuwachotsa kuti asawakumbukirenso pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nkhopeya Yehovaitsutsananao akucita zoipa, Kudula cikumbukilo cao pa dziko lapansi.