Psalms 34:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anthu ake akulira kuti aŵathandize, Chauta amamva naŵapulumutsa m'mavuto ao onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwowo anaitana, ndipo Yehova anawamva, nawalanditsa kumasautso ao onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Olungama amafuwula, ndipo Yehova amawamva; Iye amawalanditsa ku mavuto awo onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwowo anaitana, ndipo Yehova anawamva, Nawalanditsa ku masautso ao onse.