Psalms 34:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a Mulungu amaona masautso ambiri. Komabe Chauta amawapulumutsa m'mavuto awo onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masautso a wolungama mtima achuluka, koma Yehova amlanditsa mwa onsewa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wolungama atha kukhala ndi mavuto ambiri, Koma Yehova amamulanditsa ku mavuto onsewo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masautso a wolungama mtima acuruka: Koma Yehova amlanditsa mwa onsewa.