Psalms 34:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Moyo wanga umanyadira Chauta. Anthu ozunzika amve ndipo akondwere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wanga udzatamanda Yehova; ofatsa adzakumva nadzakondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Moyo wanga udzanyadira Yehova; anthu osautsidwa amve ndi kukondwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wanga udzatamanda Yehova; Ofatsa adzakumva nadzakondwera.