Psalms 34:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mngelo wa Chauta amatchinjiriza anthu omvera Iye, ndipo amaŵapulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mngelo wa Yehova azinga kuwatchinjiriza iwo akuopa Iye, nawalanditsa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngelo wa Yehova amatchinjiriza amene amakonda Iye ndi kuwalanditsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mngelo wa Yehova azinga kuwacinjiriza iwo akuopa Iye, Nawalanditsa iwo.