Psalms 35:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mboni zoipa zikundiwukira, zikundifunsa zinthu zimene sindikuzidziŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mboni za chiwawa ziuka, zindifunsa zosadziwa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mboni zopanda chisoni zinayimirira, zinandifunsa zinthu zimene sindikuzidziwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mboni za ciwawa ziuka, Zindifunsa zosadziwa ine.