Psalms 35:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine pamene adani anga analikudwala, ndidavala chiguduli kuwonetsa chisoni. Ndidadzilanga posala zakudya. Ndidapemphera nditaŵeramitsa mutu wanga pa chifuŵa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine, pakudwala iwowa, chovala changa ndi chiguduli. Ndinazunza moyo wanga ndi kusala; ndipo pemphero langa linabwera kuchifuwa changa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene iwo ankadwala, ine ndinavala chiguduli ndi kudzichepetsa ndekha posala zakudya. Pamene mapemphero anga anabwerera kwa ine osayankhidwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine, pakudwala iwowa, cobvala canga ndi ciguduli: Ndinazunza moyo wanga ndi kusala; Ndipo pemphero langa linabwera ku cifuwa canga.