Psalms 35:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine nditagwa m'mavuto, iwo aja adasonkhana akusangalala. Adandisonkhanira onse pamodzi, anthu achabechabe amene sindidaŵadziŵe nkomwe, ndipo ankangondisinjirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakutsimphina ine anakondwera, nasonkhana pamodzi; akundipanda anandisonkhanira; ndipo sindinachidziwa, ananding'amba osaleka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene ndinaphunthwa, iwo anasonkhana mosangalala; ondithira nkhondo anasonkhana kutsutsana nane, ineyo osadziwa. Iwo sanasiye kundiyankhulira mawu onyoza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakutsimphina ine anakondwera, nasonkhana pamodzi: Akundipanda anandisonkhanira; ndipo sindinacidziwa: Ananding'amba osaleka: