Psalms 35:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo ankapitirira kundinyodola mwachipongwe, namandikukutira mano ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakati pa onyodola pamadyerero, anandikukutira mano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga anthu osapembedza, iwo anandinyoza mwachipongwe; anandikukutira mano awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakati pa onyodola pamadyerero, Anandikukutira mano.