Psalms 35:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musalole kuti adani anga onyenga akondwere chifukwa cha mavuto anga, musalole kuti amene amandida popanda chifukwa, andiyang'ane cham'mbali mondinyoza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adani anga asandikondwerere ine monyenga; okwiya nane kopanda chifukwa asanditsinzinire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musalole adani anga onyenga akondwere chifukwa cha masautso anga; musalole kuti amene amadana nane popanda chifukwa andiyangʼane chamʼmbali mondinyoza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adani anga asandikondwerere ine monyenga; Okwiya nane kopanda cifukwa asanditsinzinire.