Psalms 35:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gwirani chishango ndi lihawo, ndipo fulumirani mundithandize.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Gwirani chikopa chotchinjiriza, ukani kundithandiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tengani chishango ndi lihawo; dzukani ndipo bwerani mundithandize.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Gwirani cikopa cocinjiriza, Ukani kundithandiza.