Psalms 35:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tiyeni, Inu Chauta, dzukani kuti munditchinjirize pa mlandu wanga, Inu Mulungu wanga ndi Ambuye anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Galamukani, ndipo khalani maso kundiweruzira mlandu wanga, Mulungu wanga ndi Ambuye wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzukani, ndipo nyamukani kunditeteza! Mulimbane nawo chifukwa cha ine, Mulungu wanga ndi Ambuye anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Galamukani, ndipo khalani maso kundiweruzira mlandu wanga, Mulungu wanga ndi Ambuye wanga,